Diversity Academy

Diversity Academy

yohane Mpeketula

0 좋아요2:372026년 9월 23일
Make it a gift

프롬프트

[Lumba] Eeeeya Ampeke production *[CHORUS - Yoyimba mokweza]* Diversity academy eeiiyeee Ndipamwamba. Diversity academy iyeee Ndi number one *[VERSE 1 - Kwa makolo]* Makolo nonse, mvetserani uthenga wabwino, Ku Diversity Academy, maphunziro ndi apamwamba, Aphunzitsi aluso, maphuzilo kathithi Bweretsani ana anu, tsogolo lawo lili pano Aaaaiiiiiii *[CHORUS]* Diversity academy eeiiyeee Ndipamwamba. Diversity academy iyeee Ndi number one *[VERSE 2 - Chifukwa chobweretsera ana]* Sukulu yokhaayo, yomwe imapambanitsa, Ndinzelu zapamwamba Mmmm Chingerezi cholimba, nzeru zomwe zimawala, Malipiro abwino, zotsatira zabwino nthawi zonse A aaaa eee Aziphuzitsi kuphuzitsa mwa ntims onse Kuzipeleka mwa luntha ndi nzelu zonse Maphuzilo okomela onse eiyeeee iiiii Diversity Academy, ndi number one *[BRIDGE - Mawu otsatsa]* Musachedwe, malo alipooo Zamuyeseni mwana waanuu Ndi diversity pang'ono! Pang'onooo gang'a anakweza chulu Eeee iiii a Ku diversity!!!!! mwana yo ndi number one ! *[CHORUS YOMALIZA - Yaikulu]* Diversity academy eeiiyeee (bweretsani ana!)